News
Chipasupasu! A Malawi a sambwadza Namalomba
This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. … aMalawi ali nganganga pambuyo pa Suleman Yatangwanika zedi nduna yofalitsa nkhani a Shadric Namalomba kuikira kumbuyo akuluakulu aboma pa nkhani yoti nduna ndi akuluakulu ena akususa kwambiri pa ndalama za misonkho ya a Malawi. Koma aMalawi sakugwirizana ndi ganizoli. Posachedwapa, sipikala wa nyumba ya malamulo Sameer Suleman, adayankhula pa mwambo wina kudzudzula mchitidwe waumbava […] Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Source: Malawi Nyasa ↗