News
Eagles ikudziwa kale zaife — Akidu
This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Mphunzitsi wa timu ya Ekhaya FC Fundi Akidu wati timu ya apolisi ya Standard Bank Blue Eagles ikubwera pa bwalo la Mpira ikudziwa kale kuti ikudzakumana ndi timu yabwimo. Polankhula poyembekezera masewero a lero a mu FDH Bank Premiership msabata ya chi 18, Akidu wati timu yake yakonzeka mokwana ndipo sakulora kuchinyitsa zigoli. Iye wavomereza […] Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Source: Malawi Nyasa ↗