News
Mjigo wakana kukonzedwa ku Kasungu
This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Agwidwa njakata aphunzitsi ndi ophunzira pa sukulu ya Nthema Primary, kudera la mfumu yaikulu Wimbe ku Kasungu komwe mjigo sukumva kukonzedwa. Pomwe azanyengo akulimbikitsa anthu kumwa madzi pafupifu pafupi kamba ka kutentha konyanyira, kupeza madziwa pakati pa ophunzira pa sukuluyi ndi ntchito ya padera kamba ka mjigowu omwe tsopano ndi bwenzi la mphasa. Malingana ndi […] Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.
Source: Malawi Nyasa ↗