This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.
….komabe, wati mwina mu nthawi yoyikika zidzatheka Uneneri wa mtumiki Thinos Kamanja ukuwoneka kuti kwapano waomba mgolo pomwe Norman Chisale watemetsa nkhwangwa pa mwala kuti alibe maganizo olowa m’malo mwa Peter Mutharika ngati mtsogoleri wa chipani cha DPP mu 2030. Masiku apitawo, mneneri Kamanja ananenera kuti Mulungu wamuwonetsera kuti Chisale ndi yemwe akhale mtsogoleri wa […]
Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.