Skip to main content
news Breaking News
clock

Ndale zikusokoneza ubale wa m’tsogoleri wa dziko ndi wachiwiri wake – PAC

This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Bungwe la Public Affairs Committee (PAC) lati kusagwirizana pakati pa mtsogoleri wa dziko lino ndi wa chiwiri wake, ndichitsimikizo choti m’dziko muno ndale ndizomwe zima...

Ndale zikusokoneza ubale wa m’tsogoleri wa dziko ndi wachiwiri wake – PAC

This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.

Bungwe la Public Affairs Committee (PAC) lati kusagwirizana pakati pa mtsogoleri wa dziko lino ndi wa chiwiri wake, ndichitsimikizo choti m’dziko muno ndale ndizomwe zimagwira ntchito kwambiri kuposa malamulo. Izi ndi malingana ndi woyankhulira bungwe la PAC a Bishop Gilford Matonga omwe anena izi Loweruka pomwe amayankhula ndi imodzi mwa nyumba zowulutsa mawu mdziko muno. […]

Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.

Read the full article at Malawi Nyasa

Article details
Published
November 15, 2026
Last updated
November 23, 2026
Written by
ADM Staff
Reading time
1 min read
Views
3
A
Written by

ADM Staff

Platform administrator at Afridev Monitor. Oversees the newsroom platform, user access and publishing settings, keeping the site reliable and editorially consistent. Afridev Monitor tracks development, policy and business news across Africa.

Leave a Reply

Cancel Reply

Your email address will not be published.

Please Accept Cookies for Better Performance