Skip to main content
news Breaking News
clock

Zionetsero zayima ku Mulanje

This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform. Zionetsero zomwe mzika zokhudzidwa ku Mulanje zinakonza kuti zichitike la Chiwiri likudzali pa 17 Novembela zalepheleka. Malinga ndi wapampando wagululi a Oliver Andrys a...

Zionetsero zayima ku Mulanje

This article was originally published on Malawi24, Malawi's #1 independent news platform.

Zionetsero zomwe mzika zokhudzidwa ku Mulanje zinakonza kuti zichitike la Chiwiri likudzali pa 17 Novembela zalepheleka. Malinga ndi wapampando wagululi a Oliver Andrys ati ganizoli ladza ponena kuti agwilitsa ntchito njira yokambirana potula madandaulo awo ku boma. Wapampandoyu wati ganizoli ladza kutsatira pambuyo pa zokambirana ndi anthu onse okhudzidwa m’bomali. Iye anati anthu onse okhudzidwa […]

Read the full article and more Malawi news at Malawi24 — Breaking news, politics, business, sport and entertainment from Malawi and Africa, updated 24/7.

Read the full article at Malawi Nyasa

Article details
Published
November 15, 2026
Last updated
November 23, 2026
Written by
ADM Staff
Reading time
1 min read
Views
2
A
Written by

ADM Staff

Platform administrator at Afridev Monitor. Oversees the newsroom platform, user access and publishing settings, keeping the site reliable and editorially consistent. Afridev Monitor tracks development, policy and business news across Africa.

Leave a Reply

Cancel Reply

Your email address will not be published.

Please Accept Cookies for Better Performance